Recordings
Arrangement
Chorus
Soprano | Alto | Tenor
Odi Munyumba
Odi Munyumba
Tisaimba alleluia hosanna kumwamba
Tisaimba alleluia hosanna kumwamba
Bass
Odi Odi Munyumba
Odi Odi Munyumba
Tisaimba alleluia hosanna kumwamba
Tisaimba alleluia hosanna kumwamba
Verses
Soprano | Alto
- Ntungululu ndi manja hosanna, mwamba
- Kuyamika kwachifundo hosanna, mwamba
- Kwainu akhulu oyera hosanna, mwamba
- Akhulu ndi ana omwe hosanna, mwamba
- Aluluta ndimavume hosanna, mwamba
- Chifukwa ndioyera hosanna, mwamba
- Aimba ndi azeze hosanna, mwamba
- Aimbidwa moyamika hosanna, mwamba
- Kwa Utatu anu oyera hosanna, mwamba
Tenor | Bass
kuMwamba