Recordings
Arrangement
Chorus
Soprano | Alto | Tenor | Bass
Pazabwino
Pazabwino zonse mumatichitira, yhwh
Yhwh, yhwh, yhwh inu Mulungu.
Pazabwino
Verses
Cantor
- Ndikutokozani, YHWH
- Ndikuimbirani, YHWH
- Ndikuyamikani, YHWH
- Ndikutamandani, YHWH
Pazabwino