Recordings
Arrangement
Chorus
Soprano | Alto | Bass
Ndipereka
Ndipereka moyo wanga
Ndipereka ine
Ndipereka moyo wanga
Verses
Cantor Soprano
- Ndilibe mphotso ine zopereka Kwa Mulungu wanga Ndipereka ine
- Ndilibe chuma ine chopereka Kwa Mulungu wanga Ndipereka ine
- Ndilibe mwana ine wopereka Kwa Mulungu wanga Ndipereka ine
- Ndilibe siliva ine lopereka Kwa Mulungu wanga Ndipereka ine
- Ndilibe golide ine wopereka Kwa Mulungu wanga Ndipereka ine
All (Response)
Ndipereka moyo wanga